Curriculum

Dongosolo la Maphunziro

Chaka Choyamba - Year 1

Kuona Chipangano Chakhale (Old Testament Survey)

Kuona Chipangano Chatsopano (New Testament Survey)

Moyo wa Khristu (Life of Christ)

Machitidwe a Atumwi (Acts of Apostles)

Kulalika Kwake (How to Preach)

Kukhula M'moyo wa Chikhristu (Christian Growth Course)

Chaka Chachiwiri - Year 2

Aroma ndi Agalatiya (Romans and Galatians)

1 & 2 Akorinto (1 a)nd 2 Corinthians

Mabukhu a Nyimbo (OT Books of Poetry)

Mbiri ya Mpingo (History of the Church)

Ntchito ya pa Malo a Mpingo (Work of the Local Church)

Moyo ndi Ntchito za Mlaliki (Life and Work of a Preacher)

Chaka Chachitatu - Year 3

Mabukhu a Mbiri--Gawo Loyamba (OT Books of History – Part 1)

Makalata a kwa Onse (General Letters)

Utsogoleri wa Mpingo (Church Leadership)

Kulambira kwa Mpingo (The Worship of the Church)

Mabukhu a Mbiri--Gawo Lachiwiri (OT Books of History – Part 2)

Kuphunzitsa Nyumba ndi Nyumba (Teaching House to House)

Chaka Chachinai - Year 4

Mabukhu a Ulosi (OT Books of Prophecy)

Makalata a ku Ndende (Prison Letters)

Makalata a kwa Alaliki (Letters to Preachers)

Chibvumbulutso (Revelation)

Kumasulira Malembon (How to Understand the Bible)

Banja la Chikhristu (The Christian Family)

 

Other advanced courses are offered at Namikango each year.